Umoyo FM
  • Home
  • Featured
  • Politics
  • Business
  • Entertainment
  • Lifestyle
  • Sports
  • About Us
  • Contact
  • Login
  • Umoyo FM

    ya ulimi

    UMOYOSPORTS

    ZIONETSERO ZOKAKAMIZA BOMA KUTI LIMANGE MSEWU WA MANGOCHI-MAKANJIRA ZICHTIKA LACHIWIRI LIKUBWERALI.

    Mclove MafutaJune 20, 20250199 views

    Gulu lotchedwa Mangochi-Makanjira Road Concerned Citizens lati lachiwiri pa 24 June, lichita zionetsero zofuna kukakamiza boma kuti likwaniritse lonjezano lake lomanga msewu…

    Read more

    SALIMA ATUMIKIRABE BULLETS

    Mclove MafutaJune 20, 20250125 views

    SALIMA ATUMIKIRABE FCB Timu ya mpira wa miyendo ya FCB Nyasa Big , yalengeza kuti Chikumbutso Salima akhala akutumikira ku timuyi mpaka…

    Read more

    NTCHITO YOGAWA CHIMANGA KUMAWANJA OMWE ANAONEKELEDWA NG’AMBA YAYAMBA KU MANGOCHI.

    Mclove MafutaMay 28, 20250152 views

    Mawanja omwe anavutika ndi ng’amba okwana 13,997 okhala m’madera a Makanjira ndi Lulanga ku Mangochi, akuyembekezeleka kulandira thandizo la chimanga ndi mnthambi…

    Read more

    KAMWENDO YAKE YAUMA KU CRECK SPORTING

    Mclove MafutaMay 28, 20250156 views

    Timu ya Creck Sporting yachotsa ntchito mphunzitsi wake Joseph Kamwendo ndi omuthandizira Abel Mkandawire komanso Chiukepo Msowoya. Atatuwa achotsedwa kamba ka kusachita…

    Read more

    MAKIDA NDIYEMWE ANYAMULE MCP KU MANGOCHI.

    Mclove MafutaMay 16, 20250292 views

    A Vincent Makida ndiomwe adzaimire ngati phungu wachipani cha MCP. Makida wapambana muzisankho zachipulura ndimavoti 1177 pomwe a Hassan Hussein apeza mavoti…

    Read more

    BUNGWE LA MEC LALENGEZA KUTI KUYAMBIRA SABATA LA MAWA LIKHALE LIKUCHITITSA KAUNIUNI WA ANTHU OMWE AKUDZAPONYA VOTI.

    Mclove MafutaMay 7, 20250293 views

    Bungwe loyendetsa chisankho mdziko muno la MEC lati lichitsa kauniuni wa anthu omwe ali mundandanda ozavota kuyambira lachiwiri sabata yamawa. Bungweli lalengeza…

    Read more

    MNTHUMWI ZOPOSA 100 ZAPATSIDWA UKADAULO WAMAKONO OYANG’ANIRA CHISANKHO CHAMMAIKO A SADIC

    Mclove MafutaMay 2, 20251170 views

    Mlembi wamkulu ku unduna oona zaubale wamaiko akunja (Foreign Affairs) wati ndiokhutira ndimaphunziro anthumwi zamaiko am’chigawo chakum’mwera kwa Africa (SADC) aukadaulo wamakono…

    Read more

    BUNGWE LA ESCOM LATHANDIZA AMAYI OPOSA 100 KUMAPHUNZIRO AUKADAULO WALUSO LAMANJA.

    Mclove MafutaMay 1, 20250160 views

    Bungwe lopelekera magetsi la ESCOM Limited, lati ophunzira achizimayi okwana 120 ndiomwe pakalipano la wathandiza kumaphunziro aukadaulo waluso lamanja ngati mbali imodzi…

    Read more

    NTHAMBI YA ZANKHALANGO YALANDA MATUMBA AMAKALA OKWANA 212 OPANDA CHITUPA.

    Mclove MafutaMay 1, 20250154 views

    Bambo wina wazaka 31 ku Mangochi ali m’manja mwapolisi kaamba kopezeka ndimakala opanda chilolezo. Malinga ndi mneneri wapolisi m’bomali Inspector Amina Tepan…

    Read more

    DZIKO LA MALAWI LIKUYEMBEKEZELEKA KUCHITITSA MSONKHANO WAZAMALIMIDWE WA MAIKO AMUNO MU AFRICA

    Mclove MafutaApril 30, 20250156 views

    Unduna wazamalimidwe walengeza kuti uchititsa msonkhano wachisanu ndi chiwiri (7) wasabata yapadera wamaiko amuno mu Africa(Africa-wide Agricultural Extension Week-AAEW) mwezi wamawa. Nduna…

    Read more

    Posts navigation

    1 … 8 9
    View Desktop Version

    Powered by PenciDesign

    Back To Top