CHIWELENGERO CHA ANTHU OFUNA KUDZAIMIRA PA MPANDO WA PULEZIDENTI NDIPO ALIPIRA SOPANO CHAKWANA 10
Bungwe la Malawi Electoral Commission MEC lati chiwelengero cha anthu amene alipilira K10,000 ndikutenga kalata zawo zofuna kudzaimila pa udindo wa tsogoleri…