Malawi Congress Party (MCP) is today holding a press briefing at the Party’s National Headquarters. The briefing aims to address the media …
Uncategorized
-
-
Bambo wina White Mussa wazaka 26 ku Mangochi akuyembekezereka kuyankha mlandu kaamba kopha bambo ake atasemphana maganizo pathumba la mpunga zomwe ndizosemphana …
-
Uncategorized
BOMA LAPEREKA NDALAMA ZOPOSERA K7 MILLION KUTI ZITHANDIZIRE MWAMBO WAMALIRO KWA MZIKA ZOMWE ZINAFA PANGOZI YA BUS.
Mtsogoleri wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wapereka ndalama zokwana K500,000 kwa mawanja 15 omwe achibale awo anafa pangozi ya bus ku …
-
Dalaivala wina alimmanja mwa apolisi ataomba ndikupha ana awiri m’mudzi mwa Sumaili m’boma la Mangochi. Sharifu Duwa wazaka 10 ndi Kifa Charles …
-
UmoyoSports Bungwe la Superleague Of Malawi Sulom,latulutsa mndandanda wa mmene masewero akhalire mu sabata Yoyamba mu Ligi yaikulu ya mdziko muno ya …
-
Boma lalamula ofesi ya mnthambi yopanga zitupa zolowera ndi kutulukira mdziko yamumzinda wa Blantyre (Immigration) kuti mwezi uno ukamatha ikhale yatulutsa mlingo …
-
Rising waters in Lake Malawi and the Shire River are battering Mangochi, submerging homes and drowning parts of the district’s vital tourism …
-
Security at First Vice President Justice Jane Ansah’s official residence in Lilongwe was thrown into high alert last night after a drone …
-
Mlimi wina waphedwa ndi njobvu yolusa kufupi ndi nkhalango ya Namizimu m’boma la Mangochi. Ofalitsa nkhani zapolisi m’bomali Inspector Amina Tepani Daudi, …
-
Uncategorized
A MUTHARIKA APEMPHA MGWIRIZANO PAKATI PAMAIKO AMU SADC KUTI NTCHITO ZACHITUKUKO ZIPITE PATSOGOLO.
Pulezidenti wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika yemwenso ndi mtsogoleri wamaiko am’chigawo chakum’mwera Kwa Africa (SADC) maka kumnthambi yoona zachitetezo ndi ubale, …