ATSUTSA ZOTI ASILIKALI ANDENDE AKUNYANYALA NTCHITO- PRISON SERVICE.

M’nthambi yoona zachitetezo chandende mdziko muno (Malawi Prison Service) yati posatengera mphekesera zoti asilikali ake ali ndi maganizo onyanyala ntchito, chitetezo chinakali chokhwima m’ndende zonse.

Ofalitsa nkhani ku m’nthambiyi a Steve Meke atsikimizira izi URS potsutsa mphekeserazi kuti ndizabodza ponena kuti asilikaliwa akugwira ntchito yawo popanda chovuta chilichonse.

Ndipo a Meke ati m’nthambiyi ipitiriza kugwira ntchito mwaukadaulo wawo popereka chitetezo kwa a akaidi omwe akusungidwa ndende zamdziko muno.

Related posts

MCP TO HOLD A PRESS BRIEFING AIMED TO SHARPENING THE PARTY’S FUTURE.

MKULU WINA WAPHA BAMBO AKE KAAMBA KAMPUNGA.

BOMA LAPEREKA NDALAMA ZOPOSERA K7 MILLION KUTI ZITHANDIZIRE MWAMBO WAMALIRO KWA MZIKA ZOMWE ZINAFA PANGOZI YA BUS.