Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) lati lasintha tsiku lochititsira msonkhano wa atolankhani okhudza zotsatira zachisankho.
Mneneli wa bungwe la MEC a Sangwani Mwafulirwa wati bungweli lachita izi kuti lilengeze zotsatira zonse za m’tsogoleri mawa.
A Mwafulirwa alengezanso kuti bungwe la MEC silinalandire chiletso chilichonse lero, kuti asalengeze zotsatirazi