Home Uncategorized NTCHITO YOGAWA CHIMANGA KUMAWANJA OMWE ANAONEKELEDWA NG’AMBA YAYAMBA KU MANGOCHI.

NTCHITO YOGAWA CHIMANGA KUMAWANJA OMWE ANAONEKELEDWA NG’AMBA YAYAMBA KU MANGOCHI.

by Mclove Mafuta
0 comments

Mawanja omwe anavutika ndi ng’amba okwana 13,997 okhala m’madera a Makanjira ndi Lulanga ku Mangochi, akuyembekezeleka kulandira thandizo la chimanga ndi mnthambi yoona zangozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA kuyambira lero.

Potsindikizira URS Online zadongosololi mneneri ku khonsolo ya Mangochi Bishop Witmos wati matumba achimanga okwana 13,313 adzera panyanja ya Malawi kuchokera ku Monkey-Bay pasitima ndipo matumba 684 adzera nawo pamsewu ndi galimoto la bungwe loona zachakudya padziko lonse (World Food Program -WFP).

You may also like

Leave a Comment

Dowa Community Radio is a community-based radio station established in 2020 to be used as a tool of communication in Dowa district and surrounding areas to facilitate issues of Education, gender-based violence, culture, child trafficking, Agriculture, Climate change and environment, transparency and accountability, sports, community self reliance, and many more.

Newsletter

Subscribe my Newsletter for new blog posts, tips & new photos. Let's stay updated!

@2025 – All Right Reserved. MACRA Community Radios

Are you sure want to unlock this post?
Unlock left : 0
Are you sure want to cancel subscription?
-
00:00
00:00
Update Required Flash plugin
-
00:00
00:00