MAKIDA NDIYEMWE ANYAMULE MCP KU MANGOCHI.

A Vincent Makida ndiomwe adzaimire ngati phungu wachipani cha MCP.

Makida wapambana muzisankho zachipulura ndimavoti 1177 pomwe a Hassan Hussein apeza mavoti 315 zisankho zomwe zinachitikira pa bwalo la Mangochi stadium.

Related posts

https://umoyofm.mw/tigwirizane-polimbana-ndi-hiv/

TIGWIRIZANE POLIMBANA NDI HIV

ANTHU APEMPHEDWA KUSINTHA KAGANIZIDWE PA ZAMATENDA OSAPATSIRANA.