KAMWENDO YAKE YAUMA KU CRECK SPORTING

Timu ya Creck Sporting yachotsa ntchito mphunzitsi wake Joseph Kamwendo ndi omuthandizira Abel Mkandawire komanso Chiukepo Msowoya.

Atatuwa achotsedwa kamba ka kusachita bwino kwa Timuyi yomwe ili pa nambala 11 mu ndandanda wa ma timu mu mpikisano wa TNM superleague ndi ma point 8 pamasewero 7.

Polankhula ndi URS Online Kamwendo watsimikiza zakuchotsedwa kwake ndipo wathokoza timu ya Creck Sporting pomupatsa mwayi okhala mphunzitsi wa timuyi.

Related posts

https://umoyofm.mw/tigwirizane-polimbana-ndi-hiv/

TIGWIRIZANE POLIMBANA NDI HIV

ANTHU APEMPHEDWA KUSINTHA KAGANIZIDWE PA ZAMATENDA OSAPATSIRANA.