Bungwe la Malawi Electoral Commission MEC lati chiwelengero cha anthu amene alipilira K10,000 ndikutenga kalata zawo zofuna kudzaimila pa udindo wa tsogoleri …
Uncategorized
-
-
Gulu la Mangochi Makanjira road concerned citizens lapeleka masiku khumi ndi awiri ku boma kuti lifotokoze momwe likuyendetsera dongosolo lomanga msewuwo ponena …
-
FDH Bank Cup iyamba pa 5 july2025 Mayere a chikho cha FDH Bank anachitika Lachiwiri pa 24 June, 2025 ku chiwembe Ndipo …
-
Wachiwiri kwamtsogoleri wadziko lino Dr Michael Usi wafika mdziko la Mozambique komwe akakhale nawo pamwambo okumbukira tsiku lomwe dzikolo linalandira Ufulu odzilamulira …
-
Umoyofm Coalition for Health Workers, a non-governmental organization has called all health workers to report any human rights abuses they experience in …
-
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yafika mu ndime yotsiridza ya chikho cha Airtel Top 8 itangonjetsa timu ya Karonga United ndi …
-
Uncategorized
CHIWERENGERO CHA ANTHU OMWE AONETSA CHIDWI CHODZAPIKISANA PAMPANDO WA UTSOGOLERI WADZIKO CHAFIKA PA 13.
Mtsogoleri wa chipani cha People’s Transformation (Petra) a Kamuzu Walter Chiwambo komanso a Smart Swira omwe ndioima paokha, lero atenga kalata zosonyeza …
-
Uncategorized
ZIONETSERO ZOKAKAMIZA BOMA KUTI LIMANGE MSEWU WA MANGOCHI-MAKANJIRA ZICHTIKA LACHIWIRI LIKUBWERALI.
Gulu lotchedwa Mangochi-Makanjira Road Concerned Citizens lati lachiwiri pa 24 June, lichita zionetsero zofuna kukakamiza boma kuti likwaniritse lonjezano lake lomanga msewu …
-
SALIMA ATUMIKIRABE FCB Timu ya mpira wa miyendo ya FCB Nyasa Big , yalengeza kuti Chikumbutso Salima akhala akutumikira ku timuyi mpaka …
-
Mawanja omwe anavutika ndi ng’amba okwana 13,997 okhala m’madera a Makanjira ndi Lulanga ku Mangochi, akuyembekezeleka kulandira thandizo la chimanga ndi mnthambi …