NTHAMBI YA ZANKHALANGO YALANDA MATUMBA AMAKALA OKWANA 212 OPANDA CHITUPA.
Bambo wina wazaka 31 ku Mangochi ali m’manja mwapolisi kaamba kopezeka ndimakala opanda chilolezo. Malinga ndi mneneri wapolisi m’bomali Inspector Amina Tepan…
Bambo wina wazaka 31 ku Mangochi ali m’manja mwapolisi kaamba kopezeka ndimakala opanda chilolezo. Malinga ndi mneneri wapolisi m’bomali Inspector Amina Tepan…
Unduna wazamalimidwe walengeza kuti uchititsa msonkhano wachisanu ndi chiwiri (7) wasabata yapadera wamaiko amuno mu Africa(Africa-wide Agricultural Extension Week-AAEW) mwezi wamawa. Nduna…
Mtsogoleri wakale wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika yemwenso ndi mtsogoleri wachipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP) lero akhala nawo pamwambo wamaliro…
Apolisi ku Mangochi akusunga mchitolokosi shoveli wina wa minbus kaamba kogunda ndikupha ophunzira wapasukulu yaukachenjede ya DMI wazaka 22 usiku wadzulo lolemba…
Mnthambi yoona zanyengo ndikusintha kwa nyengo (Department of Climate Change and Meteorological Services) yamema anthu okhala m’madera amphepete mwanyanja kuti akhale tcheru…
Unduna waza Umoyo mogwirizana ndi bungwe la Autism Hope Trust ndimabungwe ena wati pa 26 mwezi uno uchititsa mwambo okumbukira matenda aulumali…
The Chief Operations Officer for Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) Limited has cautioned the general public that denying assigned staff member’s…