BUNGWE LA MEC LALENGEZA KUTI KUYAMBIRA SABATA LA MAWA LIKHALE LIKUCHITITSA KAUNIUNI WA ANTHU OMWE AKUDZAPONYA VOTI.
Bungwe loyendetsa chisankho mdziko muno la MEC lati lichitsa kauniuni wa anthu omwe ali mundandanda ozavota kuyambira lachiwiri sabata yamawa. Bungweli lalengeza…