Ophunzira wina pa sukulu ya ukachenjede ya DMI ku Mangochi wafa atagundidwa ndi galimoto
Apolisi ku Mangochi akusunga mchitolokosi shoveli wina wa minbus kaamba kogunda ndikupha ophunzira wapasukulu yaukachenjede ya DMI wazaka 22 usiku wadzulo lolemba…