KAMWENDO YAKE YAUMA KU CRECK SPORTING
Timu ya Creck Sporting yachotsa ntchito mphunzitsi wake Joseph Kamwendo ndi omuthandizira Abel Mkandawire komanso Chiukepo Msowoya. Atatuwa achotsedwa kamba ka kusachita…
Timu ya Creck Sporting yachotsa ntchito mphunzitsi wake Joseph Kamwendo ndi omuthandizira Abel Mkandawire komanso Chiukepo Msowoya. Atatuwa achotsedwa kamba ka kusachita…
A Vincent Makida ndiomwe adzaimire ngati phungu wachipani cha MCP. Makida wapambana muzisankho zachipulura ndimavoti 1177 pomwe a Hassan Hussein apeza mavoti…
Bungwe loyendetsa chisankho mdziko muno la MEC lati lichitsa kauniuni wa anthu omwe ali mundandanda ozavota kuyambira lachiwiri sabata yamawa. Bungweli lalengeza…
Mlembi wamkulu ku unduna oona zaubale wamaiko akunja (Foreign Affairs) wati ndiokhutira ndimaphunziro anthumwi zamaiko am’chigawo chakum’mwera kwa Africa (SADC) aukadaulo wamakono…
Bungwe lopelekera magetsi la ESCOM Limited, lati ophunzira achizimayi okwana 120 ndiomwe pakalipano la wathandiza kumaphunziro aukadaulo waluso lamanja ngati mbali imodzi…
Bambo wina wazaka 31 ku Mangochi ali m’manja mwapolisi kaamba kopezeka ndimakala opanda chilolezo. Malinga ndi mneneri wapolisi m’bomali Inspector Amina Tepan…
Unduna wazamalimidwe walengeza kuti uchititsa msonkhano wachisanu ndi chiwiri (7) wasabata yapadera wamaiko amuno mu Africa(Africa-wide Agricultural Extension Week-AAEW) mwezi wamawa. Nduna…
Mtsogoleri wakale wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika yemwenso ndi mtsogoleri wachipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP) lero akhala nawo pamwambo wamaliro…
Apolisi ku Mangochi akusunga mchitolokosi shoveli wina wa minbus kaamba kogunda ndikupha ophunzira wapasukulu yaukachenjede ya DMI wazaka 22 usiku wadzulo lolemba…
Mnthambi yoona zanyengo ndikusintha kwa nyengo (Department of Climate Change and Meteorological Services) yamema anthu okhala m’madera amphepete mwanyanja kuti akhale tcheru…