BANJA LINA ALINJATA LITAPEZEKA NDI MFUTI YOPANDA CHILOLEZO.
Banja lina lili m’manja mwa apolisi ku Chiponde m’boma la Mangochi atalipeza ndi mfuti yamtundu wa Pistol yopanda chilolezo. Malingana ndi mneneri…
Banja lina lili m’manja mwa apolisi ku Chiponde m’boma la Mangochi atalipeza ndi mfuti yamtundu wa Pistol yopanda chilolezo. Malingana ndi mneneri…
Mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus McCathy Chakwera wayamikira bank ya Reserve (RBM) kaamba kochilimika pochepetsa mavuto akusowa kwa ndalama zakunja. Dr Chakwera…
Gulu lomwe silandale la Mkamulano wa Yao ku Mangochi, lapempha anthu okhala m’bomali kuti azasankhe phungu yemwe ali ndi mfundo zachitukuko. Wachiwiri…
Anthu pafupifupi 50,000 ali pachiopsezo choti atha osaponya nawo voti mwezi wa seputembala ngati lamulo silisintha. Wapampando wabungwe la Civil Society Elections…
The Democratic Progressive Party’s (DPP) effort to appoint one of its members, Mackford Somanje, as a commissioner at the Malawi Electoral Commission…
Mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus McCathy Chakwera wapempha anthu kukhala ololerana komanso kulemekeza ufulu wa ena pomwe nyengo ya kampeni yatsegulidwa. Dr…
Bungwe loyendetsa chisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lalengeza kuti lidzawerengera mavoti pamanja osati pamakina . Mai Justice Annabel Mtalimanja…
Mpikisano otenga kalata zosonyeza chidwi chodzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wadziko muchisankho chapa 16 September ukupitilirabe kukula pomwe lero kalata inanso…
M’nthambi yoona zachitetezo chandende mdziko muno (Malawi Prison Service) yati posatengera mphekesera zoti asilikali ake ali ndi maganizo onyanyala ntchito, chitetezo chinakali…
Bungwe loyendetsa chisankho mdziko muno la MEC lalengeza kuti lolemba pa 14 July, lichititsa mwambo waukulu okhadzikitsa masiku amisonkhano yomwe cholinga chake…