Bungwe la Center for Social Concerns (CfSC) lawalimbikitsa atolankhani a boma la Mangochi kuti azilemba nkhani zomwe zingabweretse ntendere pakati pa anthu …
June 2025
-
-
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets mogwirizana ndi banki ya FCB akonza Chikondwelero choti bankiyi yakwanitsa zaka makumi atatu(30).Ndipo mwambowu uchitike Lamulungu …
-
Uncategorized
CHIWELENGERO CHA ANTHU OFUNA KUDZAIMIRA PA MPANDO WA PULEZIDENTI NDIPO ALIPIRA SOPANO CHAKWANA 10
Bungwe la Malawi Electoral Commission MEC lati chiwelengero cha anthu amene alipilira K10,000 ndikutenga kalata zawo zofuna kudzaimila pa udindo wa tsogoleri …
-
Gulu la Mangochi Makanjira road concerned citizens lapeleka masiku khumi ndi awiri ku boma kuti lifotokoze momwe likuyendetsera dongosolo lomanga msewuwo ponena …
-
FDH Bank Cup iyamba pa 5 july2025 Mayere a chikho cha FDH Bank anachitika Lachiwiri pa 24 June, 2025 ku chiwembe Ndipo …
-
Wachiwiri kwamtsogoleri wadziko lino Dr Michael Usi wafika mdziko la Mozambique komwe akakhale nawo pamwambo okumbukira tsiku lomwe dzikolo linalandira Ufulu odzilamulira …
-
Umoyofm Coalition for Health Workers, a non-governmental organization has called all health workers to report any human rights abuses they experience in …
-
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yafika mu ndime yotsiridza ya chikho cha Airtel Top 8 itangonjetsa timu ya Karonga United ndi …
-
Uncategorized
CHIWERENGERO CHA ANTHU OMWE AONETSA CHIDWI CHODZAPIKISANA PAMPANDO WA UTSOGOLERI WADZIKO CHAFIKA PA 13.
Mtsogoleri wa chipani cha People’s Transformation (Petra) a Kamuzu Walter Chiwambo komanso a Smart Swira omwe ndioima paokha, lero atenga kalata zosonyeza …
-
Uncategorized
ZIONETSERO ZOKAKAMIZA BOMA KUTI LIMANGE MSEWU WA MANGOCHI-MAKANJIRA ZICHTIKA LACHIWIRI LIKUBWERALI.
Gulu lotchedwa Mangochi-Makanjira Road Concerned Citizens lati lachiwiri pa 24 June, lichita zionetsero zofuna kukakamiza boma kuti likwaniritse lonjezano lake lomanga msewu …