Mawanja omwe anavutika ndi ng’amba okwana 13,997 okhala m’madera a Makanjira ndi Lulanga ku Mangochi, akuyembekezeleka kulandira thandizo la chimanga ndi mnthambi …
May 2025
-
-
Timu ya Creck Sporting yachotsa ntchito mphunzitsi wake Joseph Kamwendo ndi omuthandizira Abel Mkandawire komanso Chiukepo Msowoya. Atatuwa achotsedwa kamba ka kusachita …
-
A Vincent Makida ndiomwe adzaimire ngati phungu wachipani cha MCP. Makida wapambana muzisankho zachipulura ndimavoti 1177 pomwe a Hassan Hussein apeza mavoti …
-
Uncategorized
BUNGWE LA MEC LALENGEZA KUTI KUYAMBIRA SABATA LA MAWA LIKHALE LIKUCHITITSA KAUNIUNI WA ANTHU OMWE AKUDZAPONYA VOTI.
Bungwe loyendetsa chisankho mdziko muno la MEC lati lichitsa kauniuni wa anthu omwe ali mundandanda ozavota kuyambira lachiwiri sabata yamawa. Bungweli lalengeza …
-
Uncategorized
MNTHUMWI ZOPOSA 100 ZAPATSIDWA UKADAULO WAMAKONO OYANG’ANIRA CHISANKHO CHAMMAIKO A SADIC
Mlembi wamkulu ku unduna oona zaubale wamaiko akunja (Foreign Affairs) wati ndiokhutira ndimaphunziro anthumwi zamaiko am’chigawo chakum’mwera kwa Africa (SADC) aukadaulo wamakono …
-
Bungwe lopelekera magetsi la ESCOM Limited, lati ophunzira achizimayi okwana 120 ndiomwe pakalipano la wathandiza kumaphunziro aukadaulo waluso lamanja ngati mbali imodzi …
-
Bambo wina wazaka 31 ku Mangochi ali m’manja mwapolisi kaamba kopezeka ndimakala opanda chilolezo. Malinga ndi mneneri wapolisi m’bomali Inspector Amina Tepan …