DZIKO LA MALAWI LIKUYEMBEKEZELEKA KUCHITITSA MSONKHANO WAZAMALIMIDWE WA MAIKO AMUNO MU AFRICA
Unduna wazamalimidwe walengeza kuti uchititsa msonkhano wachisanu ndi chiwiri (7) wasabata yapadera wamaiko amuno mu Africa(Africa-wide Agricultural Extension Week-AAEW) mwezi wamawa. Nduna…