Unduna wazamalimidwe walengeza kuti uchititsa msonkhano wachisanu ndi chiwiri (7) wasabata yapadera wamaiko amuno mu Africa(Africa-wide Agricultural Extension Week-AAEW) mwezi wamawa. Nduna …
Monthly Archives
April 2025
-
-
Uncategorized
MTSOGOLERI WAKALE WADZIKO LINO WALENGEZA KUTI AKHALA NAWO PAMWAMBO WAMALIRO MASANA ANO KU BALAKA
Mtsogoleri wakale wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika yemwenso ndi mtsogoleri wachipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP) lero akhala nawo pamwambo wamaliro …
-
Uncategorized
Ophunzira wina pa sukulu ya ukachenjede ya DMI ku Mangochi wafa atagundidwa ndi galimoto
Apolisi ku Mangochi akusunga mchitolokosi shoveli wina wa minbus kaamba kogunda ndikupha ophunzira wapasukulu yaukachenjede ya DMI wazaka 22 usiku wadzulo lolemba …
-
Uncategorized
LERO KUOMBA MPHEPO YOTHAMANGA MAKILOMITA 36 PAOLA ILIYONSE YATERO NTHAMBI YA ZANYENGO.
Mnthambi yoona zanyengo ndikusintha kwa nyengo (Department of Climate Change and Meteorological Services) yamema anthu okhala m’madera amphepete mwanyanja kuti akhale tcheru …
-
Uncategorized
UNDUNA WAZA UMOYO WAPEMPHA ANTHU KUTENGA NAWO MBALI POKUMBUKIRA MATENDA A ULUMALI OZELEZEKA AMU UBONGO.
Unduna waza Umoyo mogwirizana ndi bungwe la Autism Hope Trust ndimabungwe ena wati pa 26 mwezi uno uchititsa mwambo okumbukira matenda aulumali …